Tisanthule Baibulo @ ttb.twr.org/chichewa

By Thru the Bible Chichewa

Listen to a podcast, please open Podcast Republic app. Available on Google Play Store and Apple App Store.


Category: Christianity

Open in Apple Podcasts


Open RSS feed


Open Website


Rate for this podcast

Subscribers: 0
Reviews: 0
Episodes: 260

Description

Pologalamu ya Tisanthule Baibulo ndi gawo limodzi lautumiki, ophunzitsa Baibulo, otchedwa ulendo m??baibulo (Thru the Bible). Mndandanda wamapogalamuwu unakonzedwa ndi Dr. J. Vernon McGee ndipo unatanthauzidwa mu zilankhulo zoposa zana zimodzi (100). Zinakonzedwa kuti pologalamu imodzi idzikhala ya mphindi makumi atatu (30) ndipo kuti pomaliza zidzathe kuthandiza omvera kumvetsetsa Baibulo lonse. Ndipo pakali pano mapologalamu onsewa tawaika pamakina a Intaneti. Ndife oyamika kuti mwasankha kuphunzira zambiri zokhudza mau a Mulungu kudzera mmapologalamuwa. Tikukulimbikitsani kuti mudzimvera pologalamu imodzi patsiku kuyambira lolemba mpaka lachisanu. Ngati mungakwanitse kutsatira ndondomekoyi, pakutha kwa zaka zisanu mudzakhala kuti mwawerenga Baibulo lonse.

Episode Date
Miyambi ya Solomoni
Dec 12, 2025
Miyambi ya Solomoni
Dec 11, 2025
Miyambo ya Solomoni
Dec 10, 2025
Miyambi ya Solomoni
Dec 09, 2025
Miyambi ya Solomoni
Dec 08, 2025
Miyambo ya Solomoni
Dec 05, 2025
Miyambi ya Solomoni
Dec 04, 2025
Miyambi ya Solomoni
Dec 03, 2025
Miyambo ya Solomoni
Dec 02, 2025
Kusiyanitsa zinthu zabwino ndi zoipa
Dec 01, 2025
Miyambi ya Solomoni
Nov 28, 2025
Miyambi ya Solomoni
Nov 27, 2025
Kupitiliza kuona miyambo ya Solomoni
Nov 26, 2025
Kupitiliza kuona miyambi ya Solomoni
Nov 25, 2025
Miyambo ya Solomoni
Nov 24, 2025
Yesu Kristu ndiye sukulu yophunzirako nzeru
Nov 21, 2025
Kodi nzeru, nchiyani?
Nov 20, 2025
Chenjezo ku tchimo la chiwerewere/chigololo
Nov 19, 2025
Zinthu zisanu ndi ziwiri zomwe Mulungu amadananazo
Nov 18, 2025
Chiyero cha ukwati
Nov 17, 2025
Kupereka malangizo oonjezera kwa mnyamata
Nov 14, 2025
Kupitiliza kupereka malangizo kwa mnyamata
Nov 13, 2025
Malangizo ochenjeza mnyamata
Nov 12, 2025
Adani a mnyamata
Nov 11, 2025
Mnyamata ayenera kukhala ndi nzeru pamene akumana ndi zovuta
Nov 10, 2025
Malangizo kwa mnyamata amene akuyamba moyo watsopano
Nov 07, 2025
Kusanthula chiyambi cha buku la Miyambo
Nov 06, 2025
Paulo ndiye chitsanzo cha m’sirikari wabwino wa Kristu
Nov 05, 2025
Chitetezo cha mpingo ngati msirikari
Nov 04, 2025
Mpingo ngati m’sirikari uyenera kudziwa m’dani wake
Nov 03, 2025
Mpingo Uyenera Kudziwa Mdani wake
Oct 31, 2025
Mpingo uyenera kukhala msirikari wabwino wa Kristu
Oct 30, 2025
Mpingo ndiye msirikari
Oct 29, 2025
Kupitiliza kuona zochitika ndi mpingo
Oct 28, 2025
Zomwe mpingo uyenera kuchita
Oct 27, 2025
Mpingo ndiwo mkwatibwi
Oct 24, 2025
Kupitiliza kutsogolera munthu watsopano mwa Kristu
Oct 23, 2025
Kutsogolera munthu watsopano mwa Kristu
Oct 22, 2025
Zosayenera kuchita munthu watsopano
Oct 21, 2025
Mpingo ndiye munthu watsopano
Oct 20, 2025
Paulo apempherera mpingo wa ku Aefeso kuti ukhale ndi mphamvu ndi chidziwitso
Oct 17, 2025
Mpingo ndi chinthu chobisika chimene chaonetsedwa lero
Oct 16, 2025
Njira ndi tanthauzo la kumanga mpingo
Oct 15, 2025
Zipangizo ndi njira zomangira Kachisi wa Mulungu
Oct 14, 2025
Zipangazo zomangira Kachisi
Oct 13, 2025
Mpingo ukufanizidwa kachisi
Oct 10, 2025
Pemphero la Paulo kwa Aefeso
Oct 09, 2025
Mulungu Mzimu, ndiye amateteza mpingo
Oct 08, 2025
Mulungu Mwana ndiye anagula mpingo
Oct 07, 2025
Mulungu Mwana ndiye anagula mpingo
Oct 06, 2025
Mulungu ndiye anayika chikonzero cha mpingo
Oct 03, 2025
Mulungu ndiye anayika chikonzero cha mpingo
Oct 02, 2025
Madalitso auzimu
Oct 01, 2025
Paulo Apereka Malonje Ndi Chisomo Ku Mpingo wa Aefeso
Sep 30, 2025
Chiyambi Cha Kalata Yolembedwa Ku Aefeso
Sep 29, 2025
Kutamanda Mulungu chifukwa cha Umulungu wake ndi zomwe amachita
Sep 26, 2025
Kupempha kulanditsidwa kuchokera kwa anthu woipa
Sep 25, 2025
Nyimbo yotamanda Mulungu ndi mtima wonse
Sep 24, 2025
Kuyimba nyimbo za Ambuye m’dziko la chilendo
Sep 23, 2025
Ufumu wa Kristu mu Yerusalemu
Sep 22, 2025
Ana a Israyeli abwerera ku Yerusalemu
Sep 19, 2025
Moyo wa kuchilendo
Sep 18, 2025
Kulemekeza mau a Mulungu
Sep 17, 2025
Nyimbo Ya Matamando Kwa Mulungu
Sep 16, 2025
Mulungu Amatsogolera Ana Ake Okondeka
Sep 15, 2025
Kukwezedwa Kwa Kristu Pa Ntchito Za Chilungamo Cha Mulungu
Sep 12, 2025
Kukoma Kwa Mulungu; Kudzichepetsa Kwa Khristu Yesu
Sep 11, 2025
Chiyamiko Pachifundo Cha Mulungu
Sep 10, 2025
Pemphero Lothana Ndi Adani
Sep 09, 2025
Nyimbo Za Chikondwerero Ndi M’chiyero
Sep 08, 2025
Nyimbo Ya Pangano La Davide
Sep 05, 2025
Kubwezeretsedwa Kwa Israyeli
Sep 04, 2025
Oweruza Ana A Mulungu Adzaweruzidwa
Sep 03, 2025
Tsogolo La Israyeli M’nthawi Ya Masautso
Sep 02, 2025
Ulosi Wa Mesiya Pampando Wachifumu
Sep 01, 2025
Chiyero Ndi Nsembe
Aug 29, 2025
Pemphero La Chipulumutso
Aug 28, 2025
Nyimbo Ya Chiwombolo
Aug 27, 2025
Chofuna Ndi Chikhulupiriro Cha Woyera Mtima
Aug 26, 2025
Davide Achita Mantha Ndipo Adalira Pa Chifundo Ndi Chilungamo Cha Mulungu
Aug 25, 2025
Za Wotsutsana Ndi Yesu
Aug 22, 2025
Pemphero La Kulapa Kwa Davide
Aug 21, 2025
Chiweruzo Cha Odzitamandira Pa Chuma
Aug 20, 2025
Mulungu Ndiye Pothawirapo Pathu
Aug 19, 2025
Kulira Kwa Israyeli M’nthawi Ya Mazunzo
Aug 18, 2025
Chokhumba Cha Munthu Woopa Mulungu
Aug 15, 2025
Kupachikidwa Pamtanda Kwa Kristu Ndi Chiwembu Cha Yudasi
Aug 14, 2025
Chithunzi Cha Woipa Ndi Mdalitso Wa Mtsogolo
Aug 13, 2025
Nyimbo Ya Matamando Chifukwa Cha Kumasulidwa
Aug 12, 2025
Uphungu Ndi Chiyamiko
Aug 11, 2025
Pemphero La Kuomboledwa M’mabvuto
Aug 08, 2025
Liwu La Yehova Mu Mphenzi Ndi Nyimbo Yoyamika Chifukwa Cha Machiritso
Aug 07, 2025
Pemphero La Kulira M’nthawi Ya Mabvuto
Aug 06, 2025
Kupempha Chifundo Pa Chipulumutso
Aug 05, 2025
Kristu Ndiye M’busa Wamkuru, Komanso M’busa Weniweni
Aug 04, 2025
Yesu Khristu Apachikidwa
Aug 01, 2025
Kukwera Kumwamba Kwa Kristu
Jul 31, 2025
Mulungu Aonekera M’chilengedwe, M’malamulo Ndi Mwa Khristu
Jul 30, 2025
Davide Atamanda Mulungu Pomulanditsa Ku Dzanja La Sauli
Jul 29, 2025
Kuuka Kwa Mesiya
Jul 28, 2025
Masautso Ya Davide Ndi Kuipa Kwa Munthu
Jul 25, 2025
Kuyesedwa Kwa Wolungama
Jul 24, 2025
Munthu Wokana Kristu Adzalangidwa
Jul 23, 2025
Salmo La Umunthu Wa Khristu Yesu Ndi Chipambano Chake
Jul 22, 2025
Kuitana Ambuye M’masautso, Kufuna Chifundo Ndi Kubwezera Adani
Jul 21, 2025
Pemphero La M’mawa Ndi Lausiku
Jul 18, 2025
Munthu Aukira Mulungu
Jul 17, 2025
Mphamvu Ndi Kusindikizika Kwa Munthu Wolungama
Jul 16, 2025
Maziko A Buku La Masalimo Ndi Zinthu Zoyenera Kuchita Munthu Wodala
Jul 15, 2025
Kuipa Kwa Kukhala M’thupi Kuonekera Mwa Akristu Achiyuda, Ndi Zizindikiro Za Paulo Za Mtanda Wa Kristu
Jul 14, 2025
Chomwe Munthu Anafesa, Adzakolora Chomwecho
Jul 11, 2025
Kuthandizana Muuzimu Mwalamulo La Chikondi La Kristu
Jul 10, 2025
Moyo Mwa Mzimu Wa Kristu Umabereka Chipatso
Jul 09, 2025
Kulimbana Pakati Pa Thupi Ndi Mzimu
Jul 08, 2025
Chikondi Cha Mulungu Chimapangitsa Ife Kulemekeza Mulungu Pamene Tipereka Moyo Kwa Kristu
Jul 07, 2025
Kugwa Kuchoka M’chisomo
Jul 04, 2025
Kusiyana Kwa Chisomo Ndi Lamulo
Jul 03, 2025
Ukapolo, Chikondi Choyamba Cha Paulo Ndipo A Yuda Afuna Kulepheretsa Uthenga Wabwino
Jul 02, 2025
Ubwana Ndi Kukhwima Mu Uzimu
Jul 01, 2025
Kutsatira Lamulo Ndi Kopanda Phindu
Jun 30, 2025
Maziko A Cholowa, A Mkhalapakati Ndi Uchimo Wa Anthu Onse
Jun 27, 2025
Kuipa Kwa Lamulo Ndi Zotsatira Za M’pangano La Abrahamu
Jun 26, 2025
Kulungamitsidwa Mwachikhulupiriro Mwa Chitsanzo Cha Abrahamu
Jun 25, 2025
Zomwe Anachita A Galatiya
Jun 24, 2025
Munthu Amalungamitsidwa Mwachikhulupiriro
Jun 23, 2025
Zomwe Paulo Anachita Mu Yerusalemu Ndi Atumwi Ena
Jun 20, 2025
Paulo Aulula Kuti Utumiki Wake Ndi Wochokera Kwa Ambuye Yesu Kristu
Jun 19, 2025
Malonje, Kuonetsa Mutu Wotsogolera Ndi Chidzudzulo Chachikuru
Jun 18, 2025
Chiyambi Cha Bukhu Ndi Utumwi Wa Paulo
Jun 17, 2025
Mulungu Alankhulana Ndi Yobu
Jun 16, 2025
Mulungu Ndiye Mphunzitsi Wamkuru
Jun 13, 2025
Elihu Akamba Zabwino Pa Zomwe Mulungu Wachitira Yobu
Jun 12, 2025
Mulungu Amaphunzitsa Kudzera Mu Chilango
Jun 11, 2025
Elihu Adzudzula Yobu Ndi Abwenzi Ake Atatu
Jun 10, 2025
Yobu Atsiriza Kudzikanira
Jun 09, 2025
Kudzikweza Ndilo Bvuto La Yobu
Jun 06, 2025
Yobu Apitiliza Kudzilungamitsa Yekha
Jun 05, 2025
Kodi Chifukwa Ninji Anthu Woipa Amakhala M’moyo Wachisangalaro?
Jun 04, 2025
Kudzudzula Kwa Chitatu Kwa Elifazi
Jun 03, 2025
Zofari Adzudzula Kachiwiri, Ndipo Yobu Adzikanira
Jun 02, 2025
Bilidadi Adzudzula Kachiwiri, Ndipo Yobu Adzikanira
May 30, 2025
Yobu Adzudzula Abwezi Ake Kuti Sakunena Zoona Ndipo Akumuchitira Nkhaza
May 29, 2025
Elifazi Ayeseranso Kulangiza Yobu
May 28, 2025
Yobu Adzikanira Pa Chidzudzulo Cha Zofari
May 27, 2025
Yobu Akufunitsitsa Mthandizi Kapena Mkhalapakati
May 26, 2025
Bilidadi Adzudzula Yobu
May 23, 2025
Mau Opanda Pake A Elifazi Sadathandize Yobu
May 22, 2025
Elifazi Alankhula Pa Masautso Ya Wochimwa
May 21, 2025
Yobu Ayembekeza Zoipa Zina Pa Moyo Wake
May 20, 2025
Cholinga Cha Masautso A Yobu
May 19, 2025
Kuonetsedwa Zochitika M’mwamba
May 16, 2025
Chiyambi Cha Bukhu La Yobu
May 15, 2025
Kukhazikitsa Madyerero A Purimu
May 14, 2025
Uthenga Wa Chiyembekezo Wochokera Kwa Mfumu
May 13, 2025
Kusapeza Tulo Kwa Mfumu, Kunapangitsa Kuti Hamani Anadza Ku Phwando, Apachikidwe Pa Tsanja
May 12, 2025
Chiwembu Cha A Yuda Chisowetsa Mfumu Tulo
May 09, 2025
Moredekai Adandaulira Estere Anene Nkhani Ya A Yuda Kwa Mfumu
May 08, 2025
Hamani Achitira Chiwembu A Yuda
May 07, 2025
Estere Akhala Mkazi Wa Mfumu
May 06, 2025
Mpikisano Wosankha Mkazi Wa Mfumu
May 05, 2025
Mkazi Yemwe Sanamvere Mwamuna Wake Ndi Mpikisano Wosankha Chiphadzuwa
May 02, 2025
Chiyambi Cha Bukhuli Ndi Madyerero A Kunyumba Ya Chifumu
May 01, 2025
Kukwaniritsa Ndi Kumaliza Utumiki Wa Paulo
Apr 30, 2025
Kubvomerezeka Kwa Utumiki Wa Paulo
Apr 29, 2025
Kuyenerezeka Kwa Utumiki Wa Paulo
Apr 28, 2025
Zinthu Zobvomerezetsa Utumiki Wa Paulo
Apr 25, 2025
Chopereka Cha Akristu Osauka Aku Yerusalemu
Apr 24, 2025
Chitsanzo Cha Kupereka Kwa Mkristu
Apr 23, 2025
Chitsanzo Cha Kupereka Kwa Mkristu
Apr 22, 2025
Chitonthozo Cha Mulungu Kwa Paulo Payekha
Apr 21, 2025
Chitonthozo Cha Mulungu Mzinthu Zonse Pa Utumiki Wa Kristu
Apr 18, 2025
Chitonthozo Cha Mulungu Mu Nyengo Zonse Za Utumiki Wa Kristu
Apr 17, 2025
Chitonthozo Cha Mulungu Mu Utumiki Wophedwa, Wa Atumiki A Kristu
Apr 16, 2025
Kupitiliza Za Chitonthozo Cha Mulungu Pa Utumiki Wophedwa Chifukwa Cha Kristu
Apr 15, 2025
Chitonthozo Cha Mulungu Muutumiki Wa Khristu Pakuphedwa Kwa Atumiki Ake
Apr 14, 2025
Chitonthozo Cha Mulungu Pakutumikira Kristu M’masautso
Apr 11, 2025
Chitonthozo Cha Mulungu Mu Utumiki Wa Kuzunzika Chifukwa Cha Kristu
Apr 10, 2025
Chitonthozo Cha Mulungu Mu Utumiki Wa Ulemerero Wa Kristu
Apr 09, 2025
Utumiki Wopambana: Kusiyana Kwa Pangano La Kale Ndi La Tsopano
Apr 08, 2025
Chitonthozo Cha Mulungu Pakulandiranso Munthu Wokhulupirira Amene Wataika
Apr 07, 2025
Kupitiliza Kuona Chitonthozo Cha Mulungu Pa Zikonzero Za Moyo Wa Munthu
Apr 04, 2025
Chiyambi Cha Bukuli Ndi Chitonthozo Cha Mulungu Pa Zikonzero Za Moyo Uno
Apr 03, 2025
Kusintha Kwa Zinthu Kumachokera Ku Chitsitsimutso
Apr 02, 2025
Pemphero Ndiwo Maziko Achitsitsimutso
Apr 01, 2025
Ezara Atsogolera Kusanthula Baibulo
Mar 31, 2025
Nehemiya Achita Kalembera Wa Anthu
Mar 28, 2025
Linga Lamangidwa Ngakhale Adani Anali Pakati Pawo
Mar 27, 2025
Nehemiya Athana Ndi Adani A Mkati
Mar 26, 2025
Nehemiya Apemphera Chifukwa Cha M’nyozo Wa Adani Ake
Mar 25, 2025
Kumanganso Zipata Za Yerusalemu
Mar 24, 2025
Kumanganso Zipata Za Yerusalemu
Mar 21, 2025
Nehemiya Alimbikitsa Kumanganso
Mar 20, 2025
Pemphero La Nehemiya Ndipo Apempha Kubwerera Ku Yerusalemu
Mar 19, 2025
Chomukhudza Nehemiya Ndi Pemphero Lake Pa Anthu Otsala Mu Yerusalemu
Mar 18, 2025
Chitsitsimutso Motsogozedwa Ndi Ezara
Mar 17, 2025
Chitsitsimutso Pa Utsogoleri Wa Ezara
Mar 14, 2025
A Yuda Ena Abwerera Pa Utsogoleri Wa Ezara
Mar 13, 2025
Kumangidwa Kwa Kachisi Ndi Kuperekedwa
Mar 12, 2025
Kuyamba Kumanga Kachisi Ndi Kuimitsidwa
Mar 11, 2025
A Yuda Abwerera Motsogozedwa Ndi Zerubabele
Mar 10, 2025
Chiyambi Cha Bukhu La Ezra, Lamulo Ndi Kubwerera Kwa Anthu Otsala Ku Yerusalemu
Mar 07, 2025
Mau A Paulo Otsiriza, Olangiza Ndi Olimbikitsa Mpingo
Mar 06, 2025
Njira Ndi Mphamvu Ya Kuuka Kwa Akufa
Mar 05, 2025
Kuuka Kwa Akufa
Mar 04, 2025
Kufunika Kwa Kuuka Kwa Akufa Ndi Umboni Wa Kuuka Kwa Akufa Kwa Thupi La Yesu Kristu
Mar 03, 2025
Mphatso Ya Ulosi Iposa Malilime Ndi Dongosolo Pakugwiritsa Ntchito Mphatsozi
Feb 28, 2025
Chikondi Ndiyo Mphamvu Ya Mphatso Zonse
Feb 27, 2025
Woyera Kufanizidwa Ndi Thupi
Feb 26, 2025
Mphatso Za Mzimu Woyera
Feb 25, 2025
Njira Zolakwika Ndi Njira Zoyenera Pa Mgonero Wa Ambuye
Feb 24, 2025
Mwamuna Ndiulemu Wa Mulungu; Mkazi Ndiulemu Wa Mwamuna; Kutsutsana Ndi Chilengedwe Ndikuukira
Feb 21, 2025
Wokhulupira Sayenera Kutolana Cholakwa; Ukulu Wa Mulungu
Feb 20, 2025
Ufulu Wa Israyeli Sichilolezo Chopembedza Mafano
Feb 19, 2025
Ufulu Potumikira Kristu Kufikira Kukalandira Mfupo
Feb 18, 2025
Mkristu Akhale Ndi Chidziwitso Ndi Chikondi Pa M’bale Wofooka
Feb 17, 2025
Akristu Akhale Momwe Anaitanidwira Poika Yesu Kristu Patsogolo
Feb 14, 2025
Ukwati Ndi Kutha Kwa Moyo Wa Munthu- M’modzi Pa Ukwati
Feb 13, 2025
Kaweruzidwe Ka Mirandu Ya Akristu Ndi Kuchenjeza Za Uchimo
Feb 12, 2025
Chodetsa Mumpingo Wa Ku Korinto
Feb 11, 2025
Akristu Ndi Ayani; Mtanda Wa Atumwi; Kudzikweza Ndi Kudzichepetsa
Feb 10, 2025
Otsatira Yesu, Ndiwo Ogwira Ntchito M’munda Wa Mulungu, Ndiwo Akachisi A Mulungu Ndi Udindo Wapamwamba Wa Wokhulupirira
Feb 07, 2025
Nzeru Ya Mulungu; Kuunika Munthu Wachibadwidwe Ndi Wauzimu
Feb 06, 2025
Kodi Kristu Kwa Ife Ndi Yani, Kodi Ndi Wogawika?
Feb 05, 2025
Kutsimikiza Umulungu Wa Kristu, Chiyanjano, Ndi Kuletsa Magawano A Mzimu
Feb 04, 2025
Chiyambi Cha Bukhu La Akorinto
Feb 03, 2025
Ulamuliro Wa Yosiya
Jan 31, 2025
Ulamuliro Woipa Wa Manase
Jan 30, 2025
Chitsitsimutso Muulamuliro Wa Hezekiya; Kudwala Ndi Imfa Yake
Jan 29, 2025
Yuda Agonjetsedwa Ndi Syria Ndi Israyeli, Edomu Ndi Afilisti; Ndipo Chitsitsimutso Chibwera Muulamuliro Wa Hezekiya
Jan 28, 2025
Kupambana Ndi Kufooka Kwa Uziya; Ulamuliro Wa Yotamu Ndi Ahazi
Jan 27, 2025
Yowasi Abwerera M’mbuyo Pa Chipembedzo Choona; Alandira Chilango Ndi Ulamuliro Wa Amaziya
Jan 24, 2025
Kulekelera Chipembedzo Chamafano Kunadzetsa Uchimo; Chitsitsimutso Muulamuliro Wa Yowasi
Jan 23, 2025
Kubwereza Kuona Za Chitsitsimutso Cha Yehosafat; Kuputidwa Ndi Adani Komanso Kutailira Pa Nkhani Ya Uchimo
Jan 22, 2025
Kuphunzitsa Mau A Mulungu, Yehosafati Agwirizana Ndi Ahabu Ndipo Yehosafati Adzudzulidwa
Jan 21, 2025
Ulamuliro Wa Asa Usintha, Chifukwa Cha Kutsika Kwa Chikhulupiriro Chake
Jan 20, 2025
Rehabiamu Adzichepetsa Yekha; Abiya Atenga Ulamuliro Wa Yuda; Chitsitsimuka Mu Nthawi Ya Asa
Jan 17, 2025
Kugawidwa Kwa Ufumu Pansi Paulamuliro Wa Rehabiamu
Jan 16, 2025
Pemphero La Solomoni Pakupereka Kachisi; Ntchito Zake, Kutchuka Ndi Imfa Yake
Jan 15, 2025
Kumvomerezeka Kwa Kachisi Ndi Yehova
Jan 14, 2025
Kugwiritsa Ntchito Kachisi Womangidwayo
Jan 13, 2025
Kuyamba Ndi Kutsiriza Kumanga Kachisi
Jan 10, 2025
Solomoni Akhala Mfumu Ndipo Apempha Nzeru
Jan 09, 2025
Uthenga Wotsiriza Wa Davide
Jan 08, 2025
Kupitiliza Kukonzekera Za Kachisi Ndi Mau Otsiliza A Davide
Jan 07, 2025
Kupitiliza Kukonzekera Zipangizo Za Kachisi Ndikuti A Levi Akusonkhanitsidwa Kutumikira Ndi Kuimba M’kachisi
Jan 06, 2025
Dwale La Orinani Ndipo Davide Akonzekera Za Kachisi
Jan 03, 2025
Nkhondo Za Davide Ndi Uchimo Wake Pochita Kalembera Wa Anthu
Jan 02, 2025
Nkhondo Zomwe Anamenya Davide
Jan 01, 2025
Nyimbo Yoyamika Ya Davide Ndi Nkhani Ya Kachisi
Dec 31, 2024
Nkhani Ya Davide Ndi Likasa La Mulungu
Dec 30, 2024
Davide Ndi Likasa La Mulungu
Dec 27, 2024
Ulamuliro Wa Davide
Dec 26, 2024
M’ndandanda Wa Maina Ya Makolo Ndi Ulamuliro Wa Sauli
Dec 25, 2024
Chiyambi Cha Bukhu La Mbiri Ndi Kuona Za Mibadwo Ya Anthu
Dec 24, 2024
Zitsanzo Za Chikondi Chachikristu
Dec 23, 2024
Chikonzero Ndi Ndondomeko Ya Ulendo Wa Paulo
Dec 20, 2024
Paulo Apitiliza Kufotokonza Za Umboni Wa Utumiki Wake
Dec 19, 2024
A Yuda Ndi Amitundu Ali Thupi Limodzi Mwa Kristu
Dec 18, 2024
Kuthandiza M’bale Wochepa Chikhulupiriro
Dec 17, 2024
Kuonetsa Chikondi Cha Apa Abale
Dec 16, 2024